Nehemiya 4:21 - Buku Lopatulika21 Momwemo tinalikugwira ntchito; gawo lina la iwo linagwira nthungo kuyambira mbandakucha mpaka zatuluka nyenyezi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Momwemo tinalikugwira ntchito; gawo lina la iwo linagwira nthungo kuyambira mbandakucha mpaka zatuluka nyenyezi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Choncho enafe tinkagwira ntchito, ndipo theka lina la anthuwo linkagwira zida zankhondo, kuyambira m'matandakucha mpaka nyenyezi zitaoneka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Choncho enafe tinapitiriza kugwira ntchito, pamene theka lina linkanyamula mikondo kuyambira mʼbandakucha mpaka nyenyezi zitaoneka. Onani mutuwo |