Nehemiya 4:18 - Buku Lopatulika18 ndi omanga linga aliyense anamangirira lupanga lake m'chuuno mwake, nagwira ntchito motero. Ndipo woomba lipenga anali ndi ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 ndi omanga linga aliyense anamangirira lupanga lake m'chuuno mwake, nagwira ntchito motero. Ndipo woomba lipenga anali ndi ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Mmisiri aliyense anali atamangirira lupanga m'chiwuno mwake pamene ankamanga. Munthu woimba lipenga anali pambali panga nthaŵi zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mʼmisiri aliyense ankamangirira lupanga lake mʼchiwuno mwake akamagwira ntchito. Koma munthu woyimba lipenga anali pambali panga nthawi zonse. Onani mutuwo |