Nehemiya 4:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo kunali, atamva Sanibalati kuti tinalikumanga lingali, kudamuipira, nakwiya kwakukulu, naseka Ayuda pwepwete. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo kunali, atamva Sanibalati kuti tinalikumanga lingali, kudamuipira, nakwiya kwakukulu, naseka Ayuda pwepwete. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pamene Sanibalati adamva kuti tikumanga khoma, adapsa mtima nakalipa kwambiri, ndipo adayamba kuŵaseka Ayuda monyodola. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Sanibalati atamva kuti tikumanganso khoma anapsa mtima nayamba kuseka ndi kunyogodola Ayuda kwambiri. Onani mutuwo |