Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 3:28 - Buku Lopatulika

28 Kumtunda kwa Chipata cha Akavalo anakonza ansembe, yense pandunji pa nyumba yake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Kumtunda kwa chipata cha akavalo anakonza ansembe, yense pandunji pa nyumba yake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Kuyambira ku Chipata cha Akavalo, ansembe ena ankakonza khoma, aliyense moyang'anana ndi nyumba yake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Kuyambira ku Chipata cha Akavalo anakonza ndi ansembe ena ndipo aliyense amakonza khoma loyangʼanana ndi nyumba yake.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 3:28
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anamgwira, napita naye njira yolowera akavalo kunyumba ya mfumu, namupha pomwepo.


Ndipo anampisa malo; namuka iye kolowera ku Chipata cha Akavalo kunyumba ya mfumu; ndi pomwepo anamupha.


Ndi pambali pao anakonza Yedaya mwana wa Harumafa, pandunji pa nyumba yake. Ndi pambali pake anakonza Hatusi mwana wa Hasabineya.


Potsatizana nao anakonza Benjamini ndi Hasubu pandunji pa nyumba pao. Potsatizana nao anakonza Azariya mwana wa Maaseiya mwana wa Ananiya pafupi pa nyumba yake.


Potsatizana nao anakonza Zadoki mwana wa Imeri pandunji pa nyumba yake. Ndi potsatizana naye anakonza Semaya mwana wa Sekaniya, wosunga Chipata cha Kum'mawa.


Ndipo chigwa chonse cha mitembo, ndi cha phulusa, ndi minda yonse kufikira kumtsinje wa Kidroni, kufikira kungodya kwa Chipata cha Akavalo kuloza kum'mawa, ponsepo padzapatulikira Yehova; sipadzazulidwa, sipadzagwetsedwa konse kunthawi zamuyaya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa