Nehemiya 3:29 - Buku Lopatulika29 Potsatizana nao anakonza Zadoki mwana wa Imeri pandunji pa nyumba yake. Ndi potsatizana naye anakonza Semaya mwana wa Sekaniya, wosunga Chipata cha Kum'mawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Potsatizana nao anakonza Zadoki mwana wa Imeri pandunji pa nyumba yake. Ndi potsatizana naye anakonza Semaya mwana wa Sekaniya, wosunga chipata cha kum'mawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Pambali pa iwowo Zadoki, mwana wa Imeri, adakonza chigawo china choyang'anananso ndi nyumba yake. Pambali pa iyeyo Semaya, mwana wa Sekaniya, amene ankasunga Chipata chakuvuma, adakonza chigawo china. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Motsatana nawo, Zadoki mwana wa Imeri anakonza chigawo china choyangʼanana ndi nyumba yake. Motsatana naye, Semeya mwana wa Sekaniya, mlonda wa Chipata cha Kummawa, anakonzanso khoma. Onani mutuwo |