Nehemiya 3:27 - Buku Lopatulika27 Potsatizana nao Atekowa anakonza gawo lina, pandunji pa nsanja yaikulu yosomphoka ndi kulinga la Ofele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Potsatizana nao Atekowa anakonza gawo lina, pandunji pa nsanja yaikulu yosomphoka ndi kulinga la Ofele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Pambali pa Pedaya ndi anzake, Atekowa adakonza chigawo china choyang'anana ndi nsanja ija yaikulu ndi yaitali mpaka kukafika ku khoma la Ofele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Motsatana nawo, anthu a ku Tekowa anakonzanso chigawo china choyangʼanana ndi nsanja ija yayikulu ndi yayitali mpaka ku khoma la Ofeli. Onani mutuwo |