Nehemiya 3:24 - Buku Lopatulika24 Potsatizana naye Binuyi mwana wa Henadadi anakonza gawo lina, kuyambira kunyumba ya Azariya kufikira popindirira kufikira kungodya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Potsatizana naye Binuyi mwana wa Henadadi anakonza gawo lina, kuyambira kunyumba ya Azariya kufikira popindirira kufikira kungodya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Pambali pa iyeyo Binuyi, mwana wa Henadadi, adakonza chigawo china, kuyambira ku nyumba ya Azariya mpaka kukafika ku Ndonyo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Motsatana naye, Binuyi mwana wa Henadadi anakonzanso chigawo china, kuchokera pa nyumba ya Azariya kukafika potsirizira pa ngodya. Onani mutuwo |