Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 3:2 - Buku Lopatulika

2 Ndi pambali pake anamanga amuna a ku Yeriko. Ndi pambali pao anamanga Zakuri mwana wa Imuri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndi pambali pake anamanga amuna a ku Yeriko. Ndi pambali pao anamanga Zakuri mwana wa Imuri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Anthu a ku Yeriko adamanga chigawo china pambalipa, ndipo Zakuri, mwana wa Imuri, adamanga chigawo chinanso kuyandikana ndi chimenechi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Anthu a ku Yeriko anamanga chigawo china pambali pake ndipo Zakuri mwana wa Imuri anamanga chigawo chinanso choyandikana nawo.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 3:2
4 Mawu Ofanana  

Ana a Yeriko, mazana atatu mphambu makumi anai kudza asanu.


Zakuri, Serebiya, Sebaniya,


Ndi Chipata cha Nsomba anachimanga ana a Hasena; anamanga mitanda yake, ndi kuika zitseko zake, zokowera zake, ndi mipingiridzo yake.


Ana a Yeriko, mazana atatu mphambu makumi anai kudza asanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa