Nehemiya 3:3 - Buku Lopatulika3 Ndi Chipata cha Nsomba anachimanga ana a Hasena; anamanga mitanda yake, ndi kuika zitseko zake, zokowera zake, ndi mipingiridzo yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndi chipata chansomba anachimanga ana a Hasena; anamanga mitanda yake, ndi kuika zitseko zake, zokowera zake, ndi mipingiridzo yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 A fuko la Hasena adamanga Chipata cha Nsomba. Iwowo adayala mitanda yake naikira zitseko zake, zotsekera zake, ndi mipiringidzo yake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Chipata cha Nsomba chinamangidwanso ndi ana a fuko la Hasena. Iwo anayika mitanda yake ndi zitseko, zotsekera zake, ndi mipiringidzo yake. Onani mutuwo |