Nehemiya 3:18 - Buku Lopatulika18 Potsatizana naye anakonza abale ao, Bavai mwana wa Henadadi, mkulu wa dera lina la dziko la Keila. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Potsatizana naye anakonza abale ao, Bavai mwana wa Henadadi, mkulu wa dera lina la dziko la Keila. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pambali pa iyeyo abale ao adapitiriza kukonza. Mtsogoleri wao anali Bavai mwana wa Henadadi, wolamulira theka la dera lina la Keila. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pambuyo pa iyeyu abale awo anapitiriza kukonza, ndipo mtsogoleri wawo anali Bawai mwana wa Henadadi, wolamulira theka lina la chigawo cha Keyila. Onani mutuwo |