Nehemiya 3:12 - Buku Lopatulika12 Ndi pambali pake anakonza Salumu mwana wa Halohesi, mkulu wa dera lina la dziko la Yerusalemu, iye ndi ana ake akazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndi pambali pake anakonza Salumu mwana wa Halohesi, mkulu wa dera lina la dziko la Yerusalemu, iye ndi ana ake akazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pambali pa iyeyo Salumu, mwana wa Halohesi, wolamulira theka lina la dera la mzinda wa Yerusalemu, adakonza chigawo china, iyeyo pamodzi ndi ana ake aakazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Salumu mwana wa Halohesi wolamulira theka la chigawo cha Yerusalemu, anakonzanso chigawo chotsatana nawo mothandizidwa ndi ana ake akazi. Onani mutuwo |