Nehemiya 3:11 - Buku Lopatulika11 Malikiya mwana wa Harimu, ndi Hasubu mwana wa Pahatimowabu, anakonza gawo lina, ndi Nsanja ya Ng'anjo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Malikiya mwana wa Harimu, ndi Hasubu mwana wa Pahatimowabu, anakonza gawo lina, ndi Nsanja ya Ng'anjo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Malikiya, mwana wa Harimu, ndiponso Hasubu mwana wa Pahatimowabu, adakonza chigawo china pamodzi ndi Nsanja ya Ng'anjo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Malikiya mwana wa Harimu ndi Hasubu mwana wa Pahati-Mowabu anakonzanso chigawo china ndiponso Nsanja ya Ngʼanjo. Onani mutuwo |