Nehemiya 2:7 - Buku Lopatulika7 Ndinanenanso kwa mfumu, Chikakomera mfumu, indipatse makalata kwa ziwanga za tsidya lija la mtsinje, andilole ndipitirire mpaka ndifikira ku Yuda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndinanenanso kwa mfumu, Chikakomera mfumu, indipatse akalata kwa ziwanga za tsidya lija la mtsinje, andilole ndipitirire mpaka ndifikira ku Yuda; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tsono ndidauza mfumu kuti, “Ngati chingakukondweretseni amfumu, mundipatse makalata oti ndikapereke kwa abwanamkubwa a chigawo cha Patsidya pa Yufurate, kuti akandilole kudzera m'chigawocho mpaka ndikafike ku Yuda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ndipo ndinatinso kwa mfumu, “Ngati zikondweretse mfumu, mundipatse makalata oti ndikapereke kwa abwanamkubwa a ku chigawo cha Patsidya pa Yufurate, kuti akandilole kudutsa mwamtendere mpaka nditakafika ku Yuda. Onani mutuwo |