Nehemiya 2:16 - Buku Lopatulika16 Koma olamulira sanadziwe uko ndinamuka, kapena chochita ine; sindidauzenso kufikira pamenepo Ayuda, kapena ansembe, kapena aufulu, kapena olamulira, kapena otsala akuchita ntchitoyi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma olamulira sanadziwe uko ndinamuka, kapena chochita ine; sindidauzenso kufikira pamenepo Ayuda, kapena ansembe, kapena aufulu, kapena olamulira, kapena otsala akuchita ntchitoyi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Akuluakulu aja sadadziŵe kumene ndidaapita kapenanso zimene ndinkachita. Ndinali ndisanaŵauze Ayuda, ansembe, atsogoleri, akuluakulu aja kapenanso ena onse amene ankayenera kudzagwira ntchitoyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Akuluakulu sanadziwe kumene ndinapita kapena zimene ndimachita, chifukwa pa nthawiyi nʼkuti ndisananene kalikonse kwa Ayuda kapena ansembe, anthu olemekezeka kapena akuluakulu, kapena wina aliyense amene anali woyenera kugwira ntchitoyi. Onani mutuwo |