Nehemiya 2:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo ndinakwera usiku kumtsinje, ndi kuyang'ana lingali; ndinabwerera tsono ndi kulowa pa Chipata cha ku Chigwa, momwemo ndinabwereranso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo ndinakwera usiku kumtsinje, ndi kuyang'ana lingali; ndinabwerera tsono ndi kulowa pa Chipata cha ku Chigwa, momwemo ndinabwereranso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Choncho ndidayenda ndi usiku kudzera ku chigwa, kunka ndikuliyang'ana khomalo. Ndipo ndidapotoloka nkudzaloŵa mu mzinda kudzera pa Chipata cha ku Chigwa chija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Kotero usikuwo ndinapita ku chigwa, ndikuyangʼana khomalo. Pomaliza ndinabwerera ndi kukalowanso mu mzinda kudzera ku Chipata cha ku Chigwa. Onani mutuwo |