Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 13:8 - Buku Lopatulika

8 Ndipo ndinaipidwa nacho kwambiri, motero ndinataya kubwalo akatundu onse a m'nyumba ya Tobiya, kuwachotsa m'chipindamo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo ndinaipidwa nacho kwambiri, motero ndinataya kubwalo akatundu onse a m'nyumba ya Tobiya, kuwachotsa m'chipindamo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Pamenepo ndidapsa mtima kwambiri, ndipo ndidamtaya kunja katundu yense wa Tobiya amene anali m'chipindamo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Ndinapsa mtima kwambiri ndipo ndinataya kunja katundu yense wa Tobiya amene anali mʼchipindamo.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 13:8
7 Mawu Ofanana  

Pakupemphera Ezara tsono, ndi kuwulula ndi kulira misozi, ndi kudzigwetsa pansi pakhomo pa nyumba ya Mulungu, udamsonkhanira mwa Israele msonkhano waukulu ndithu wa amuna, ndi akazi, ndi ana; popeza anthu analira kulira kwakukulu.


Pamenepo ndinalamulira, ndipo anayeretsa zipindazo; ndipo ndinabwezeramonso zipangizo za nyumba ya Mulungu, pamodzi ndi zopereka za ufa ndi lubani.


Ndipo pakumva kulira kwao, ndi mau ao, kunandiipira kwambiri.


Pakuti changu cha pa nyumba yanu chandidya; ndi zotonza za iwo otonza Inu zandigwera ine.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa