Nehemiya 13:7 - Buku Lopatulika7 ndipo ndinafika ku Yerusalemu, ndi kuzindikira choipa anachichita Eliyasibu, chifukwa cha Tobiya, ndi kumkonzera chipinda m'mabwalo a nyumba ya Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 ndipo ndinafika ku Yerusalemu, ndi kuzindikira choipa anachichita Eliyasibu, chifukwa cha Tobiya, ndi kumkonzera chipinda m'mabwalo a nyumba ya Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 ndipo ndidabwereranso ku Yerusalemu. Tsono ndidapeza cholakwa chimene Eliyasibu adaachita pomkonzera Tobiya chipinda m'mabwalo a Nyumba ya Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 ndipo ndinabwerera ku Yerusalemu. Kumeneko ndinamva za chinthu choyipa chimene Eliyasibu anachita pomupatsa Tobiya chipinda mʼbwalo la Nyumba ya Mulungu. Onani mutuwo |