Nehemiya 13:6 - Buku Lopatulika6 Koma pochitika ichi chonse sindinkakhale ku Yerusalemu; pakuti chaka cha makumi atatu ndi chachiwiri cha Arita-kisereksesi mfumu ya Babiloni ndinafika kwa mfumu, ndipo atapita masiku ena ndinapempha mfumu indilole; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Koma pochitika ichi chonse sindinakhala ku Yerusalemu; pakuti chaka cha makumi atatu ndi chachiwiri cha Arita-kisereksesi mfumu ya Babiloni ndinafika kwa mfumu, ndipo atapita masiku ena ndinapempha mfumu indilole; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Pamene zimenezi zinkachitika ku Yerusalemu, nkuti ine palibe, popeza kuti pa chaka cha 32 cha ufumu wa Arita-kisereksesi, mfumu ya ku Babiloni, ine ndidaapita kwa mfumuyo. Patapita nthaŵi ndithu, ndidapempha chilolezo kwa mfumu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Koma pamene izi zonse zinkachitika mu Yerusalemu, ine kunalibe popeza mʼchaka cha 32 cha Aritasasita mfumu ya Babuloni ine ndinabwerera kwa mfumu. Patapitanso nthawi ndinapempha chilolezo kwa mfumuyo Onani mutuwo |