Nehemiya 13:9 - Buku Lopatulika9 Pamenepo ndinalamulira, ndipo anayeretsa zipindazo; ndipo ndinabwezeramonso zipangizo za nyumba ya Mulungu, pamodzi ndi zopereka za ufa ndi lubani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pamenepo ndinalamulira, ndipo anayeretsa zipindazo; ndipo ndinabwezeramonso zipangizo za nyumba ya Mulungu, pamodzi ndi zopereka za ufa ndi lubani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsono ndidalamula kuti ayeretse zipindazo. Kenaka ndidabwezeranso ziŵiya za m'Nyumba ya Mulungu, pamodzi ndi zopereka za chakudya ndi lubani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndinalamulira kuti ayeretse zipinda, ndipo kenaka ndinabwezeramo zida za mʼNyumba ya Mulungu, pamodzi ndi chopereka cha zakudya ndi lubani. Onani mutuwo |
ndi kuti tidzabwera nazo za mtanda wa mkate wathu woyamba, ndi nsembe zathu zokwera, ndi zipatso za mtengo uliwonse, vinyo, ndi mafuta, kwa ansembe, kuzipinda za nyumba ya Mulungu wathu; ndi limodzi la magawo khumi la nthaka yathu kwa Alevi; pakuti Alevi amene amalandira limodzilimodzi la magawo khumi m'midzi yonse yolima ife.