Nehemiya 13:4 - Buku Lopatulika4 Chinkana ichi, Eliyasibu wansembe, woikidwa asunge zipinda za nyumba ya Mulungu wathu, anachita chibale ndi Tobiya, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Chinkana ichi, Eliyasibu wansembe, woikidwa asunge zipinda za nyumba ya Mulungu wathu, anachita chibale ndi Tobiya, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma zimenezi zisanachitike, wansembe Eliyasibu anali atasankhidwa kuti aziyang'anira zipinda zosungira katundu m'Nyumba ya Mulungu. Chifukwa chomvana ndi Tobiya, iyeyo Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Izi zisanachitike, wansembe Eliyasibu anali atasankhidwa kukhala woyangʼanira zipinda zosungiramo katundu za Nyumba ya Mulungu. Iyeyu ankagwirizana kwambiri ndi Tobiya. Onani mutuwo |