Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 13:30 - Buku Lopatulika

30 Momwemo ndinawayeretsa kuwachotsera achilendo onse, ndi kuikira udikiro ansembe ndi Alevi, yense kuntchito yake;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Momwemo ndinawayeretsa kuwachotsera achilendo onse, ndi kuikira udikiro ansembe ndi Alevi, yense kuntchito yake;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Umu ndimo m'mene ndidaŵayeretsera anthu poŵachotsera kalikonse kachilendo. Ndipo ndidakhazikitsa ntchito za ansembe ndi za Alevi, kuti aliyense adziŵe bwino ntchito yake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Motero ndinayeretsa ansembe ndi Alevi powachotsera kalikonse kachilendo. Ndipo ndinakhazikitsa ntchito zawo, kuti aliyense akhale pa ntchito yake.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 13:30
5 Mawu Ofanana  

Koma ife, Yehova ndiye Mulungu wathu, sitinamsiye Iye; ndi ansembe tili nao akutumikira Yehova ana a Aroni, ndi Alevi, m'ntchito mwao,


ndi kuti sitidzapereka ana athu aakazi kwa mitundu ya anthu a m'dziko, kapena kutengera ana athu aamuna ana ao aakazi;


Ndipo ansembe ndi Alevi anadziyeretsa okha, nayeretsa anthu, ndi zipata, ndi linga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa