Nehemiya 13:18 - Buku Lopatulika18 Sanatero kodi makolo anu, ndipo Mulungu wathu anatifikitsira ife ndi mzinda uno choipa ichi chonse? Koma inu muonjezera Israele mkwiyo pakuipsa Sabata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Sanatero kodi makolo anu, ndipo Mulungu wathu anatifikitsira ife ndi mudzi uno choipa ichi chonse? Koma inu muonjezera Israele mkwiyo pakuipsa Sabata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Makolo anu adachitanso motero momwemu, ndipo Mulungu wathu adadzetsa chiwonongeko pa ife ndi pa mzinda uno. Koma inu mukufuna kuutsanso mkwiyo wa Chauta pa Aisraele, pamene mukuipitsa tsiku la sabata motere.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Makolo anu anachita zomwezi ndipo Mulungu wathu anadzetsa mavuto pa ife ndi pa mzinda uwu. Kodi inu mukufuna kuwutsanso mkwiyo wa Mulungu pa Israeli pamene mukudetsa tsiku la Sabata?” Onani mutuwo |