Nehemiya 13:17 - Buku Lopatulika17 Pamenepo ndinatsutsana nao aufulu a Yuda, ndinanena nao, Chinthu chanji choipa ichi muchichita, ndi kuipsa nacho tsiku la Sabata? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Pamenepo ndinatsutsana nao aufulu a Yuda, ndinanena nao, Chinthu chanji choipa ichi muchichita, ndi kuipsa nacho tsiku la Sabata? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Pomwepo ndidadzudzula atsogoleri a Ayuda, ndipo ndidaŵafunsa kuti, “Monga simukuzindikira choipa chimene mukuchitachi pakuipitsa tsiku la sabata chonchi? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Ndipo ndinadzudzula anthu olemekezeka a dziko la Yuda. Ndinawafunsa kuti, “Nʼchoyipa chanji mukuchitachi, kumayipitsa tsiku la Sabata chotere? Onani mutuwo |