Nehemiya 12:9 - Buku Lopatulika9 Ndi Bakibukiya ndi Uni, abale ao, anawayang'anira maulonda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndi Bakibukiya ndi Uni, abale ao, anawayang'anira maulonda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Abale ao, Bakibukiya ndi Uni, ankaimba molandizana nawo pa nthaŵi ya chipembedzo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Abale awo, Bakibukiya ndi Uri, ankayimba nyimbo molandizana. Onani mutuwo |