Nehemiya 12:10 - Buku Lopatulika10 Ndi Yesuwa anabala Yoyakimu, ndi Yoyakimu anabala Eliyasibu ndi Eliyasibu anabala Yoyada, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndi Yesuwa anabala Yoyakimu, ndi Yoyakimu anabala Eliyasibu ndi Eliyasibu anabala Yoyada, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Yesuwa adabereka Yoyakimu, Yoyakimu adabereka Eliyasibu, Eliyasibu adabereka Yoyada, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Yesuwa anabereka Yowakimu, Yowakimu anabereka Eliyasibu, Eliyasibu anabereka Yoyada. Onani mutuwo |