Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 12:11 - Buku Lopatulika

11 ndi Yoyada anabala Yonatani, ndi Yonatani, anabala Yaduwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 ndi Yoyada anabala Yonatani, ndi Yonatani, anabala Yaduwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Yoyada adabereka Yonatani ndipo Yonatani adabereka Yaduwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Yoyada anabereka Yonatani, ndipo Yonatani anabereka Yaduwa.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 12:11
3 Mawu Ofanana  

Ndi Yesuwa anabala Yoyakimu, ndi Yoyakimu anabala Eliyasibu ndi Eliyasibu anabala Yoyada,


Ndi m'masiku a Yoyakimu ansembe aakulu a nyumba za makolo ndiwo: wa Seraya, Meraya; wa Yeremiya, Hananiya;


M'masiku a Eliyasibu, Yoyada, Yohanani, ndi Yaduwa, Alevi analembedwa akulu a nyumba za makolo; ansembe omwe, mpaka ufumu wa Dariusi wa ku Persiya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa