Nehemiya 12:12 - Buku Lopatulika12 Ndi m'masiku a Yoyakimu ansembe aakulu a nyumba za makolo ndiwo: wa Seraya, Meraya; wa Yeremiya, Hananiya; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndi m'masiku a Yoyakimu ansembe aakulu a nyumba za makolo ndiwo: wa Seraya, Meraya; wa Yeremiya, Hananiya; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pa nthaŵi ya Yoyakimu, mkulu wa ansembe, atsogoleri a mabanja a ansembe anali aŵa: Mtsogoleri wa fuko la Seraya anali Meraya. Wa fuko la Yeremiya, anali Hananiya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pa nthawi ya Yowakimu, awa ndiwo anali atsogoleri a mabanja a ansembe: Mtsogoleri wa fuko la Seraya anali Meraya; wa fuko la Yeremiya anali Hananiya; Onani mutuwo |