Nehemiya 12:13 - Buku Lopatulika13 wa Ezara, Mesulamu; wa Amariya, Yehohanani; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 wa Ezara, Mesulamu; wa Amariya, Yehohanani; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Wa fuko la Ezara anali Mesulamu, wa fuko la Amariya anali Yehohanani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 wa fuko la Ezara anali Mesulamu; wa fuko la Amariya anali Yehohanani; Onani mutuwo |
Ndipo Ezara mlembi anaima pa chiunda cha mitengo adachimangira msonkhanowo; ndi pambali pake padaima Matitiya, ndi Sema, ndi Anaya, ndi Uriya, ndi Hilikiya, ndi Maaseiya, kudzanja lamanja lake; ndi kudzanja lamanzere Pedaya, ndi Misaele, ndi Malikiya, ndi Hasumu, ndi Hasibadana, Zekariya, ndi Mesulamu.