Nehemiya 12:25 - Buku Lopatulika25 Mataniya, ndi Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni, Akubu, ndiwo odikira akulonda pa nyumba za chuma zili kuzipata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Mataniya, ndi Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni, Akubu, ndiwo odikira akulonda pa nyumba za chuma zili kuzipata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Mataniya, Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni ndi Akubu, anali olonda nyumba zosungiramo chuma pa zipata za ku Nyumba ya Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Mataniya, Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni ndi Akubu anali olonda nyumba zosungiramo chuma pa zipata za ku Nyumba ya Mulungu. Onani mutuwo |
Ndipo anaika monga mwa chiweruzo cha Davide atate wake zigawo za ansembe ku utumiki wao, ndi Alevi ku udikiro wao, kulemekeza Mulungu, ndi kutumikira pamaso pa ansembe, monga munayenera tsiku ndi tsiku; odikira omwe monga mwa zigawo zao ku chipata chilichonse; pakuti momwemo Davide munthu wa Mulungu adamuuza.