Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 12:26 - Buku Lopatulika

26 Awa anakhala m'masiku a Yoyakimu mwana wa Yesuwa, mwana wa Yozadaki, ndi m'masiku a Nehemiya kazembe, ndi a Ezara wansembe mlembiyo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Awa anakhala m'masiku a Yoyakimu mwana wa Yesuwa, mwana wa Yozadaki, ndi m'masiku a Nehemiya kazembe, ndi a Ezara wansembe mlembiyo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Ameneŵa ndiwo adaalipo pa nthaŵi ya Yoyakimu mwana wa Yesuwa, mwana wa Yozadaki, ndiponso pa nthaŵi ya bwanamkubwa Nehemiya ndi wansembe Ezara amene analinso katswiri wa malamulo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Iwo ndiwo ankatumikira pa nthawi ya Yowakimu mwana wa Yesuwa mwana wa Yozadaki, ndiponso pa nthawi ya bwanamkubwa Nehemiya ndi wansembe Ezara amene analinso mlembi.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 12:26
5 Mawu Ofanana  

Ndipo analamulira mafumu onse kuyambira ku Yufurate kufikira ku dziko la Afilisti, ndi ku malire a ku Ejipito.


Malemba a kalatayo mfumu Arita-kisereksesi anampatsa Ezara wansembe mlembi, ndiye mlembi wa mau a malamulo a Yehova, ndi malemba ake kwa Israele, ndi awa:


Ezara amene anakwera kuchokera ku Babiloni, ndiye mlembi waluntha m'chilamulo cha Mose, chimene Yehova Mulungu wa Israele adachipereka; ndipo mfumu inampatsa chopempha iye chonse, monga linamkhalira dzanja la Yehova Mulungu wake.


Ndipo anthu onse anasonkhana ngati munthu mmodzi kukhwalala lili ku Chipata cha Madzi, namuuza Ezara mlembi atenge buku la chilamulo cha Mose, chimene Yehova adalamulira Israele.


Ndipo Nehemiya, ndiye kazembe, ndi Ezara wansembe mlembiyo, ndi Alevi ophunzitsa anthu, ananena ndi anthu onse, Lero ndilo lopatulikira Yehova Mulungu wanu, musamachita maliro, musamalira misozi. Popeza anthu onse analira misozi pakumva mau a chilamulo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa