Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 12:23 - Buku Lopatulika

23 Ana a Levi, akulu a nyumba za makolo, analembedwa m'buku la machitidwe, mpaka masiku a Yohanani mwana wa Eliyasibu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ana a Levi, akulu a nyumba za makolo, analembedwa m'buku la machitidwe, mpaka masiku a Yohanani mwana wa Eliyasibu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Adzukulu a Levi, makamaka atsogoleri a mabanja ao, adalembedwa m'buku la Mbiri, mpaka pa nthaŵi ya Yohanani mwana wa Eliyasibu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Zidzukulu za Levi, makamaka atsogoleri a mabanja awo analembedwa mʼbuku la mbiri mpaka pa nthawi ya Yohanani mwana wa Eliyasibu.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 12:23
3 Mawu Ofanana  

M'masiku a Eliyasibu, Yoyada, Yohanani, ndi Yaduwa, Alevi analembedwa akulu a nyumba za makolo; ansembe omwe, mpaka ufumu wa Dariusi wa ku Persiya.


Ndi akulu a Alevi: Hasabiya, Serebiya, ndi Yesuwa mwana wa Kadimiyele, ndi abale ao openyana nao, kulemekeza ndi kuyamika, monga mwa lamulo la Davide munthu wa Mulungu, alonda kupenyana alonda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa