Nehemiya 12:22 - Buku Lopatulika22 M'masiku a Eliyasibu, Yoyada, Yohanani, ndi Yaduwa, Alevi analembedwa akulu a nyumba za makolo; ansembe omwe, mpaka ufumu wa Dariusi wa ku Persiya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 M'masiku a Eliyasibu, Yoyada, Yohanani, ndi Yaduwa, Alevi analembedwa akulu a nyumba za makolo; ansembe omwe, mpaka ufumu wa Dariusi wa ku Persiya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Pa nthaŵi ya Eliyasibu, Yoyada, Yohanani ndi Yaduwa, amene anali akulu a ansembe, padalembedwa maina a atsogoleri a mabanja a Alevi ndi a ansembe, mpaka pa nthaŵi imene mfumu Dariusi wa ku Persiya ankalamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Pa nthawi ya Eliyasibu, Yoyada, Yohanani ndi Yaduwa panalembedwa atsogolera a mabanja a Alevi ndi a ansembe mpaka pa nthawi ya ulamuliro wa Dariyo Mperisi. Onani mutuwo |