Nehemiya 11:9 - Buku Lopatulika9 Ndi Yowele mwana wa Zikiri ndiye woyang'anira wao, ndi Yuda mwana wa Hasenuwa ndiye wothandizana naye, poyang'anira mzinda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndi Yowele mwana wa Zikiri ndiye woyang'anira wao, ndi Yuda mwana wa Hasenuwa ndiye wothandizana naye, poyang'anira mudzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Yowele, mwana wa Zikiri, ndiye amene anali kapitao wao. Ndipo Yuda mwana wa Hasenuwa anali kapitao wachiŵiri wa mumzindamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Yoweli mwana wa Zikiri ndiye anali mtsogoleri wawo, ndipo Yuda mwana wa Hasenuya ndiye amayangʼanira chigawo cha chiwiri cha mzinda. Onani mutuwo |