Nehemiya 11:8 - Buku Lopatulika8 Ndi wotsatana naye Gabai, Salai, mazana asanu ndi anai mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndi wotsatana naye Gabai, Salai, mazana asanu ndi anai mphambu makumi awiri kudza asanu ndi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Achibale ake anali Gabai ndi Salai. Onse pamodzi analipo 928. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Abale ake anali Gabayi ndi Salaya. Onse pamodzi anali 928. Onani mutuwo |