Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 11:36 - Buku Lopatulika

36 Ndi magawo a Levi anakhala ena ku Yuda, ndi ena ku Benjamini.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Ndi magawo a Levi anakhala ena ku Yuda, ndi ena ku Benjamini.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Magulu ena a Alevi amene ankakhala m'dziko la Yuda adasamukira ku dziko la Benjamini.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Magulu ena a Alevi a ku Yuda ankakhala ku Benjamini.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 11:36
5 Mawu Ofanana  

Kutembereredwe kukwiya kwao, chifukwa kunali koopsa; ndi kupsa mtima kwao, chifukwa kunali kwankhalwe. Ndidzawagawanitsa mu Yakobo. Ndidzabalalitsa iwo mu Israele.


Lodi, ndi Ono, chigwa cha amisiri.


Ndipo ansembe ndi Alevi amene anakwera ndi Zerubabele mwana wa Sealatiele, ndi Yesuwa, ndi awa: Seraya, Yeremiya, Ezara,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa