Nehemiya 11:31 - Buku Lopatulika31 Ana a Benjamini omwe, kuyambira ku Geba pa Mikimasi, ndi Aya, ndi pa Betele ndi midzi yake, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ana a Benjamini omwe, kuyambira ku Geba pa Mikimasi, ndi Aya, ndi pa Betele ndi milaga yake, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Anthu a fuko la Benjamini nawonso adakhala kuyambira ku Geba, kubzola mpaka ku Mikimasi, Aiya, Betele ndi midzi yake, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Nazonso zidzukulu za Benjamini zinkakhala mʼdera lawo kuyambira ku Geba mpaka ku Mikimasi, Ayiya, Beteli ndi midzi yake, Onani mutuwo |