Nehemiya 11:23 - Buku Lopatulika23 Pakuti mfumu inalamulira za iwowa, naikira oimbira chowathandiza, yense chake pa tsiku lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Pakuti mfumu inalamulira za iwowa, naikira oimbira chowathandiza, yense chake pa tsiku lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Pakuti mfumu idaalamula kuti magulu oimbawo azikhalapo tsiku ndi tsiku, potsogolera maimbidwe a nyimbo za m'Nyumba ya Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Pakuti mfumu inalamula kuti tsiku ndi tsiku pa nthawi zachipembedzo oyimba nyimbowo azikhalapo. Onani mutuwo |