Nehemiya 11:21 - Buku Lopatulika21 Koma antchito a m'kachisi anakhala mu Ofele, ndi Ziha, ndi Gisipa anali oyang'anira antchito a m'kachisi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Koma Anetini anakhala m'Ofele, ndi Ziha, ndi Gisipa anali oyang'anira Anetini. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma anthu otumikira ku Nyumba ya Mulungu ankakhala ku Ofele, mu Yerusalemu, ndipo Ziha ndi Gisipa ankaŵayang'anira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Koma antchito a ku Nyumba ya Mulungu ankakhala pa phiri la Ofeli, ndipo Ziha ndi Gisipa ndiwo anali kuwayangʼanira. Onani mutuwo |