Nehemiya 11:20 - Buku Lopatulika20 Ndi Aisraele otsala ndiwo ansembe ndi Alevi, anakhala m'midzi yonse ya Yuda, yense m'cholowa chake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndi Aisraele otsala ndiwo ansembe ndi Alevi, anakhala m'midzi yonse ya Yuda, yense m'cholowa chake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Aisraele ena ndiponso ansembe ndi Alevi otsala anali m'midzi ya Yuda ndipo aliyense ankakhala m'dera la choloŵa chake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Aisraeli ena onse pamodzi ndi ansembe ndi Alevi ankakhala mʼmizinda ya Yuda, ndipo aliyense ankakhala mʼdera la makolo ake. Onani mutuwo |