Nehemiya 11:19 - Buku Lopatulika19 Ndi odikira: Akubu, Talimoni, ndi abale ao akulindira pazipata, ndiwo zana limodzi mphambu makumi asanu ndi awiri kudza awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndi odikira: Akubu, Talimoni, ndi abale ao akulindira pazipata, ndiwo zana limodzi mphambu makumi asanu ndi awiri kudza awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Alonda a ku Nyumba ya Mulungu anali aŵa: Akubu, Talimoni ndiponso achibale ao onse pamodzi analipo 172. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Alonda a ku Nyumba ya Mulungu anali awa: Akubu, Talimoni ndi abale awo. Onse pamodzi anali 172. Onani mutuwo |