Nehemiya 11:18 - Buku Lopatulika18 Alevi onse m'mzinda wopatulikawo ndiwo mazana awiri mphambu makumi asanu ndi atatu kudza anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Alevi onse m'mudzi wopatulikawo ndiwo mazana awiri mphambu makumi asanu ndi atatu kudza anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Alevi onse amene ankakhala mu mzinda wopatulika analipo 284 pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Alevi onse amene anali mu mzinda woyera analipo 284. Onani mutuwo |