Nehemiya 10:9 - Buku Lopatulika9 Ndi Alevi ndiwo Yesuwa mwana wa Azaniya, Binuyi wa ana a Henadadi, Kadimiyele; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndi Alevi ndiwo Yesuwa mwana wa Azaniya, Binuyi wa ana a Henadadi, Kadimiyele; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Alevi anali aŵa: Yesuwa mwana wa Azaniya, Binuyi, wa fuko la Henadadi, Kadimiyele, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Alevi anali awa: Yesuwa mwana wa Azaniya, Binuyi wa fuko la Henadadi, Kadimieli, Onani mutuwo |