Nehemiya 10:1 - Buku Lopatulika1 Okhomera chizindikiro tsono ndiwo Nehemiya, Tirisata mwana wa Hakaliya, ndi Zedekiya, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Okomera chizindikiro tsono ndiwo Nehemiya, Tirisata mwana wa Hakaliya, ndi Zedekiya, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Anthu amene adasindikiza chidindo chao movomereza chipanganocho ndi aŵa: Nehemiya, bwanamkubwa uja, mwana wa Hakaliya, Zedekiya, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Amene anasindikiza chidindo anali awa: Nehemiya, bwanamkubwa uja, mwana wa Hakaliya. Zedekiya, Onani mutuwo |