Nehemiya 9:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo mwa ichi chonse tichita pangano lokhazikika, ndi kulilemba, ndi akulu athu, Alevi athu, ndi ansembe athu, alikhomera chizindikiro. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo mwa ichi chonse tichita pangano lokhazikika, ndi kulilemba, ndi akulu athu, Alevi athu, ndi ansembe athu, alikomera chizindikiro. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Chifukwa cha zonsezi tikuchita chipangano chotsimikizika chichita kulemba, ndipo akuluakulu athu, Alevi athu ndi ansembe athu asindikiza chidindo pa chipanganocho. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 “Chifukwa cha zonsezi, ife tikuchita mgwirizano wokhazikika, pochita kulemba, ndipo atsogoleri athu, Alevi athu ndi ansembe athu asindikiza chidindo chawo pa mgwirizanowo.” Onani mutuwo |