Nehemiya 1:9 - Buku Lopatulika9 koma mukabwerera kudza kwa Ine, ndi kusunga malamulo anga, ndi kuwachita, angakhale otayika anu anali ku malekezero a thambo, ndidzawasonkhanitsa kuchokera komweko, ndi kubwera nao kumalo ndinawasankha kukhalitsako dzina langa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 koma mukabwerera kudza kwa Ine, ndi kusunga malamulo anga, ndi kuwachita, angakhale otayika anu anali ku malekezero a thambo, ndidzawasonkhanitsa kuchokera komweko, ndi kubwera nao kumalo ndinawasankha kukhalitsako dzina langa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma mukabwerera kwa Ine, mukamvera malamulo anga ndi kuŵatsatadi, ndiye kuti ngakhale anthu anu omwazikawo akhale kutali chotani, ndidzaŵasonkhanitsa kuchokera ku mbali zonse ndi kubwera nawo ku malo amene ndidasankha kuti azidzandipembedza kumeneko.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Koma mukabwerera kwa Ine, mukamvera malamulo anga ndi kuwatsatadi, ndiye kuti ngakhale anthu anu atabalalika kutali chotani, Ine ndidzawasonkhanitsa kuchokera kumeneko ndi kubwera nawo ku malo amene ndinasankha kuti azidzayitanira dzina langa.’ Onani mutuwo |