Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 1:8 - Buku Lopatulika

8 Mukumbukire mau mudalamulira mtumiki wanu Mose, ndi kuti, Mukalakwa, ndidzakubalalitsani mwa mitundu ya anthu;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Mukumbukire mau mudalamulira mtumiki wanu Mose, ndi kuti, Mukalakwa, ndidzakubalalitsani mwa mitundu ya anthu;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Kumbukirani mau amene mudauza Mose mtumiki wanu akuti, ‘Ngati mukhala osakhulupirika, ndidzakumwazani pakati pa anthu a mitundu ina.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 “Kumbukirani mawu amene munawuza mtumiki wanu Mose akuti, ‘Ngati mukhala osakhulupirika, ndidzakubalalitsani pakati pa mitundu ina.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 1:8
10 Mawu Ofanana  

Kumbukirani mau a kwa mtumiki wanu, amene munandiyembekezetsa nao.


Ndipo ndidzakumwaza mwa amitundu, ndi kukubalalitsa m'maiko, ndi kukuthera zodetsa zako zikuchokere.


Chifukwa chake atate adzadya ana pakati pako, ndi ana adzadya atate ao; ndipo ndidzachita maweruzo mwa iwe, ndi akutsala onse ndidzawabalalitsa kumphepo zonse.


Koma ndidzasiyapo otsala, popeza mudzakhala nao ena akupulumuka lupanga mwa amitundu pobalalitsidwa inu m'maiko maiko.


Kuchitira atate athu chifundo, ndi kukumbukira pangano lake lopatulika;


Ndipo Yehova adzakubalalitsani mwa mitundu yonse ya anthu, kuyambira malekezero a dziko lapansi kufikira malekezero a dziko lapansi; ndipo kumeneko mudzatumikira milungu ina, imene simunaidziwe, inu ndi makolo anu, yamitengo ndi yamiyala.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa