Mlaliki 9:6 - Buku Lopatulika6 Chikondi chao ndi mdano wao ndi dumbo lao lomwe zatha tsopano; ndipo nthawi yamuyaya sagawa konse kanthu kalikonse kachitidwe pansi pano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Chikondi chao ndi mdano wao ndi dumbo lao lomwe zatha tsopano; ndipo nthawi yamuyaya sagawa konse kanthu kalikonse kachitidwe pansi pano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Chikondi chao, chidani chao ndi nsanje yao, zonse zidatha kale. Ndipo pa zonse zochitika pansi pano sadzalandirako kanthu konse mpakampaka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Chikondi chawo, chidani chawo ndiponso nsanje yawo, zonse zinatha kalekale; sadzakhalanso ndi gawo pa zonse zochitika pansi pano. Onani mutuwo |