Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 9:4 - Buku Lopatulika

4 Pakuti woyang'ana ndi amoyo onse ali nacho chiyembekezo; pakuti galu wamoyo aposa mkango wakufa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Pakuti woyang'ana ndi amoyo onse ali nacho chiyembekezo; pakuti galu wamoyo aposa mkango wakufa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Komabe amene ali ndi moyo ali nacho chikhulupiriro. Paja akuti ndiponi galu wamoyo kuposa mkango wakufa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Aliyense amene ali ndi moyo amakhala ndi chiyembekezo, pajatu galu wamoyo aposa mkango wakufa!

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 9:4
7 Mawu Ofanana  

Pakuti chiyembekezo cha wonyoza Mulungu nchiyani pomlikhatu Mulungu, pomchotsera moyo wake?


Ichi ndi choipa m'zonse zichitidwa pansi pano, chakuti kanthu kamodzi kagwera onse; indetu, mtimanso wa ana a anthu wadzala udyo, ndipo misala ili m'mtima wao akali ndi moyo, ndi pamenepo apita kwa akufa.


Pakuti amoyo adziwa kuti tidzafa; koma akufa sadziwa kanthu bii, sadzalandira mphotho; pakuti angoiwalika.


Pakuti kunsi kwa manda sikungakuyamikeni Inu; imfa singakulemekezeni; Otsikira kudzenje sangaziyembekeze zoona zanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa