Mlaliki 8:2 - Buku Lopatulika2 Nditi, Sunga mau a mfumu, makamaka m'kulumbira Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Nditi, Sunga mau a mfumu, makamaka m'kulumbira Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Uzimvera lamulo la mfumu, ndipo chifukwa cha lumbiro lako kwa Mulungu usade nkhaŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ine ndikuti, mvera lamulo la mfumu, chifukwa unalumbira pamaso pa Mulungu. Onani mutuwo |