Mlaliki 7:6 - Buku Lopatulika6 Pakuti kuseka kwa chitsiru kunga minga ilikuthetheka pansi pa mphika; ichinso ndi chabe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Pakuti kuseka kwa chitsiru kunga minga ilikuthetheka pansi pa mphika; ichinso ndi chabe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Kuseka kwa zitsiru kuli ngati kuthetheka kwa moto kunsi kwa mbiya. Zimenezinso nzachabechabe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kuseka kwa zitsiru kuli ngati kuthetheka kwa moto kunsi kwa mʼphika, izinso ndi zopandapake. Onani mutuwo |